Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zefaniya 2:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo dziko la kunyanja lidzakhala la otsala a nyumba ya Yuda; adzadyetsa zoweta zao pamenepo; madzulo adzagona m'nyumba za Asikeloni; pakuti Yehova Mulungu wao adzawazonda, nadzabweza undende wao.

Werengani mutu wathunthu Zefaniya 2

Onani Zefaniya 2:7 nkhani