Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoweli 2:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzacitika kuti ali yense adzaitana pa dzina la Yehova adzapulumutsidwa; pakuti m'phiri la Ziyoni ndi m'Yerusalemu mudzakhala cipulumutso, monga Yehova anatero, ndi mwa otsala amene Yehova adzawaitana.

Werengani mutu wathunthu Yoweli 2

Onani Yoweli 2:32 nkhani