Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoweli 2:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mudzadyaidya ndi kukhuta, nimudzalemekeza dzina la Yehova Mulungu wanu, amene anacita nanu modabwiza; ndi anthu anga sadzacita manyazi nthawi zonse.

Werengani mutu wathunthu Yoweli 2

Onani Yoweli 2:26 nkhani