Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoweli 2:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma ndidzakucotserani kutali nkhondo ya kumpoto, ndi kulingira ku dziko louma ndi lopasuka, a kumaso kwace ku nyanja ya kum'mawa, ndi a kumbuyo kwace ku nyanja ya kumadzulo; ndi kununkha kwace kudzakwera, ndi pfungo lace loipa lidzakwera; pakuti inacita zazikuru.

Werengani mutu wathunthu Yoweli 2

Onani Yoweli 2:20 nkhani