Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoweli 1:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cosiya cimbalanga, dzombe lidacidya; ndi cosiya dzombe, cirimamine adacidya; ndi cosiya cirimamine, anoni adacidya.

Werengani mutu wathunthu Yoweli 1

Onani Yoweli 1:4 nkhani