Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoweli 1:19-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. Ndipfuulira kwa Inu Yehova, pakuti moto wapsereza mabusa a m'cipululu, ndi malawi a moto anatentha mitengo yonse ya kuthengo,

20. inde nyama za kuthengo zilira kwa Inu; pakuti mitsinje yamadzi yaphwa, ndi moto wapsereza mabusa a m'cipululu.

Werengani mutu wathunthu Yoweli 1