Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 9:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akalonga ananena nao, Akhale ndi moyo; ndipo anasanduka akutema nkhuni, ndi otungira madzi msonkhano wonse; monga akalonga adanena nao.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 9

Onani Yoswa 9:21 nkhani