Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 8:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Panalibe mau amodzi a zonse adazilamulira Mose osawerenga Yoswa pamaso pa msonkhano wonse wa Israyeli, ndi akazi ndi ang'ono, ndi alendo akuyenda pakati pao.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 8

Onani Yoswa 8:35 nkhani