Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 8:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Aisrayeli onse, ndi akuru ao, ndi akapitao ao, ndi oweruza ao anaima cakuno ndi cauko ca likasa, pamaso pa ansembe Alevi, akusenza likasa la cipangano la Yehova, mbadwa ndi alendo omwe; ena a iwo pandunji pa phiri la Gerizimu, ndi ena pandunji pa phiri la Ebala; monga Mose, mtumiki wa Yehova, adalamulira poyamba pala kuti adalitse anthu a Israyeli,

Werengani mutu wathunthu Yoswa 8

Onani Yoswa 8:33 nkhani