Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 8:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu ya ku Ai, anampacika pamtengo mpaka madzulo; koma polowa dzuwa Yoswa analamulira kuti atsitse mtembo wace pamtengo; ndipo anauponya polowera pa cipata ca mudzi; nauniikako mulu waukuru wamiyala, mpaka lero lino.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 8

Onani Yoswa 8:29 nkhani