Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 8:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, atatha Israyeli kupha nzika zonse za ku Ai, kuthengo, kucipululu kumene anawapitikitsira, natha onse kugwa ndi lupanga lakuthwa mpaka adathedwa onse, Aisrayeli onse anabwerera ku Ai, naukantha ndi lupanga lakuthwa.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 8

Onani Yoswa 8:24 nkhani