Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 8:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, pamene mfumu ya ku Ai anaciona, anafulumira iwo, nalawira mamawa, naturuka amuna a m'mudzi kuthirana ndi Israyeli, iye ndi anthu ace onse, poikidwiratu patsogolo pa cidikha; popeza sanadziwa kuti amlalira kukhonde kwa mudzi.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 8

Onani Yoswa 8:14 nkhani