Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 8:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi anthu onse a nkhondo okhala naye anakwera, nayandikira nafika pamaso pa mudzi, namanga misasa kumpoto kwa Ai; koma pakati pa iye ndi Ai panali cigwa.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 8

Onani Yoswa 8:11 nkhani