Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 7:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa anati, Ha! Ambuye, Yehova, mwaolotseranji anthu awa pa Yordano, kutipereka ife m'dzanja la Aamori, kutiononga ife? mwenzi titalola ndi kukhala tsidya lija la Yordano!

Werengani mutu wathunthu Yoswa 7

Onani Yoswa 7:7 nkhani