Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 7:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamene ndinaona pazofunkha maraya abwino a ku Babulo, ndi masekeli mazana awiri a siliva, ndi cikute cagolidi, kulemera kwace masekeli makumi asanu, ndinazikhumbira ndi kuzitenga; ndipo taonani, ndazibisa m'nthaka pakati pa hema wanga, ndi siliva pansi pacepo.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 7

Onani Yoswa 7:21 nkhani