Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 7:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma m'mawa adzakuyandikitsani, pfuko ndi pfuko; ndipo kudzali kuti pfukoli Yehova aliulula lidzayandikira mwa zibale zace; ndi cibale Yehova aciulula cidzayandikira monga mwa a nyumba ace; ndi a m'nyumbawo Yehova awaulula adzayandikira mmodzi mmodzi.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 7

Onani Yoswa 7:14 nkhani