Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 6:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anyamata ozondawo analowa, naturutsa Rahabi, ndi atate wace ndi mai wace ndi abale ace, ndi onse anali nao; anaturutsanso acibale ace onse; nawaika kunja kwa cigono ca Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 6

Onani Yoswa 6:23 nkhani