Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 6:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu anapfuula, naliza mphalasa ansembe; ndipo kunali, pamene anthu anamva kulira kwa mphalasa, anapfuula anthu ndi mpfuu yaikuru, niligwa linga pomwepo; nakwera anthu kulowa m'mudzi, yense kumaso kwace; nalanda mudziwo.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 6

Onani Yoswa 6:20 nkhani