Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 6:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ansembe asanu ndi awiri, akunyamula mphalasa zisanu ndi ziwiri zanyanga za nkhosa zamphongo ndi kutsogolera nazo likasa la Yehova, anayenda ciyendere naliza mphalasazo; ndi okonzeka kunkhondowo anawatsogolera, ndi akudza m'mbuyo anatsata likasa la Yehova, ansembe ali ciombere poyenda iwo.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 6

Onani Yoswa 6:13 nkhani