Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 5:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, pamene mafumu onse a Aamori okhala tsidya la kumadzulo la Yordano, ndi mafumu onse a Akanani okhala ku Nyanja ya Mcere anamvakuti Yehova anaphwetsa madzi a Yordano pamaso pa ana a Israyeli mpaka titaoloka, mtima wao unasungunuka, analibenso moyo cifukwa ca ana a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 5

Onani Yoswa 5:1 nkhani