Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 4:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Israyeli anacita monga Yoswa anawalamulira, nasenza miyala khumi ndi iwiri pakati pa Yordano, monga Yehova adalankhula ndi Yoswa, monga mwa kuwerenga kwa mapfuko a ana a Israyeli; ndipo anaoloka nayo kumka kogona, naiika komweko.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 4

Onani Yoswa 4:8 nkhani