Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 4:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Yehova Mulungu wanu anaphwetsa madzi a Yordano pamaso panu, mpaka mutaoloka; monga Yehova Mulungu wanu anacitira Nyanja Yofiira, imene anaiphwetsa pamaso pathu, mpaka titaoloka;

Werengani mutu wathunthu Yoswa 4

Onani Yoswa 4:23 nkhani