Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 3:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene iwo akusenza likasa anafika ku Yordano, nathibika m'mphepete mwa madzi mapazi a ansembe akusenza likasa, pakuti Yordano asefuka m'magombe ace onse, nyengo yonse ya masika,

Werengani mutu wathunthu Yoswa 3

Onani Yoswa 3:15 nkhani