Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 3:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzakhala, akaima mapazi a ansembe akusenza likasa la Yehova Ambuye wa dziko lonse, m'madzi a Yordano, adzadulidwa madziwo, ndiwo madzi ocokera kumagwero, nadzaima mulu umodzi.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 3

Onani Yoswa 3:13 nkhani