Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 24:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ndinakulowetsani inu m'dziko la Aamori okhala tsidya lija la Yordano; nagwirana nanu iwowa; ndipo ndinawapereka m'dzanja lanu, nimunalandira dziko lao likhale lanu lanu; ndipo ndinawaononga pamaso panu.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 24

Onani Yoswa 24:8 nkhani