Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 24:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mafupa a Yosefe amene ana a Israyeli anakwera nao kucokera ku Aigupto anawaika ku Sekemu, pa kadziko kamene adakagula Yakobo kwa ana a Hamori atate wa Sekemu ndi kuwapatsa ndalama zana; ndipo anakhala colowa ca ana a Yosefe.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 24

Onani Yoswa 24:32 nkhani