Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 24:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa anati kwa anthu, Simukhoza inu kutumikira Yehova pakuti ndiye Mulungu woyera, ndi Mulungu wansanje; sadzalekerera zolakwa zanu, kapena zocimwa zanu.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 24

Onani Yoswa 24:19 nkhani