Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 24:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinakupatsani dziko limene simunagwiramo nchito, ndi midzi simunaimanga, ndipo mukhala m'mwemo; mukudya za m'minda yamphesa, ndi minda yaazitona imene simunaioka.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 24

Onani Yoswa 24:13 nkhani