Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 24:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo munaoloka Yordano, ndi kufika ku Yeriko; ndi eni ace a ku Yeriko anaponyana nanu nkhondo, Aamori, ndi Aperizi, ndi Akanani, ndi Ahiti, ndi Agirigasi, Ahivi ndi Ayebusi; ndipo ndinawapereka m'dzanja lanu.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 24

Onani Yoswa 24:11 nkhani