Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 23:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo atapita masiku ambiri, Yehova atapumulitsa Israyeli kwa adani ao onse akuwazungulira, ndipo Yoswa adakalamba nakhala wa zaka zambiri;

2. Yoswa anaitana Aisrayeli onse, akulu akulu ao, ndi akuru ao, ndi oweruza ao, ndi akapitao ao, nanena nao, Ndakalamba, ndine wa zaka zambiri;

Werengani mutu wathunthu Yoswa 23