Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 22:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mauwo anakomera ana a Israyeli pamaso pao; ndi ana a Israyeli analemekeza Mulungu, osanenanso za kuwakwerera ndi kuwathira nkhondo, kuliononga dziko lokhalamo ana a Rubeni ndi ana a Gadi.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 22

Onani Yoswa 22:33 nkhani