Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 21:44-45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

44. Ndipo Yehova anawapatsa mpumulo pozungulira ponse, monga mwa zonse adalumbirira makolo ao; ndipo pamaso pao sipanaima munthu mmodzi wa adani ao onse; Yehova anapereka adani ao onse m'manja mwao.

45. Sikadasowa kanthu konse ka zinthu zokoma zonse Yehova adazinenera nyumba ya Israyeli; zidacitika zonse.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 21