Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 21:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapatsa kwa mabanja a ana a Merari, otsala a Alevi, motapira pa pfuko la Zebuloni, Yokineamu ndi mabusa ace, ndi Karita ndi mabusa ace,

Werengani mutu wathunthu Yoswa 21

Onani Yoswa 21:34 nkhani