Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 21:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo motapira pa pfuko la Nafitali, Kedesi m'Galileya ndi mabusa ace, ndiwo mudzi wopulumukirako wakupha mnzaceyo, ndi Hamotidori ndi mabusa ace, ndi Karitani ndi mabusa ace, midzi itatu.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 21

Onani Yoswa 21:32 nkhani