Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 2:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu ya Yeriko inatuma wina kwa Rahabi, ndi kuti, Turutsa amunawo anafika kwanu, amene analowa m'nyumba mwako; popeza anadzera kulizonda dziko lonse.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 2

Onani Yoswa 2:3 nkhani