Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 2:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza tidamva kuti Yehova anaphwetsa madzi a m'Nyanja Yofiira pamaso panu, muja mudaruruka m'Aigupto; ndi cija munacitira mafumu awiri a Aamori okhala tsidya la Yordano, ndiwo Sihoni ndi Ogi, amene mudawaononga konse.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 2

Onani Yoswa 2:10 nkhani