Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 18:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo malire analembedwa nazungulira ku mbali ya kumadzulo kumka kumwela, kucokera ku phiri pokhala patsogolo pa Beti-horoni, kumwela kwace; ndi maturukiro ace anali ku Kiriyatibaala, womwewo ndi Kiriyati-Yearimu, mudzi wa ana a Yuda; ndiyo mbali ya kumadzulo.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 18

Onani Yoswa 18:14 nkhani