Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 17:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'Isakara ndi m'Aseri Manase anali nao Betiseani ndi midzi yace, ndi Ibleamu ndi midzi yace, ndi nzika za Doro ndi midzi yace, ndi nzika za Eni-doro ndi midzi yace, ndi nzika za Taanaki ndi midzi yace, ndi nzika za Megido ndi midzi yace; dziko la mapiri atatu.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 17

Onani Yoswa 17:11 nkhani