Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 14:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinali ine wa zaka makumi anai muja Mose mtumiki wa Yehova anandituma kucokera ku Kadesi-Barinea, kukazonda dziko; ndipo ndinambwezera mau, monga momwe anakhala mumtima mwanga.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 14

Onani Yoswa 14:7 nkhani