Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 13:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo m'cigwa Betiharamu, ndi Beti-nimra, ndi Sukoti, ndi Zafoni, cotsala ca ufumu wa Sihoni mfumu ya Hesiboni, Yoidano ndi malire ace, mpaka malekezero a nyanja ya Kinereti, tsidya lija la Yordano kum'mawa.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 13

Onani Yoswa 13:27 nkhani