Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 13:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo malire a ana a Rubeni ndiwo Yordano ndi malire ace. Ndico colandira ca ana a Rubeni monga mwa mabanja ao, midzi yace ndi miraga yace.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 13

Onani Yoswa 13:23 nkhani