Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 13:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi midzi yonse ya kucidikha, ndi ufumu wonse wa Sihoni mfumu ya Aamori, wocita ufumu m'Hesiboni, amene Mose anamkantha pamodzi ndi akalonga a Midyani, Evi, ndi Rekemu, ndi Zuri, ndi Huri ndi Reba, akalonga a Sihoni, nzika za m'dziko.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 13

Onani Yoswa 13:21 nkhani