Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 13:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa anakalamba, wa zaka zambiri; ndipo Yehova ananena naye, Wakalamba, wa zaka zambiri, ndipo latsala dziko lalikurukuru, alilandire colowa cao,

Werengani mutu wathunthu Yoswa 13

Onani Yoswa 13:1 nkhani