Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 12:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sihoni mfumu ya Aaroori wokhala m'Hesiboni, wocita ufumu kuyambira ku Aroeri ndiwo m'mphepete mwa cigwa ca Arinoni, ndi pakati pa cigwa ndi pa Gileadi wogawika pakati, kufikira mtsinje wa Yaboki, ndiwo malire a ana a Amoni;

Werengani mutu wathunthu Yoswa 12

Onani Yoswa 12:2 nkhani