Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 11:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yehova anati kwa Yoswa, Usaope cifukwa ca iwowa; pakuti mawa, dzuwa lino ndidzawapereka onse ophedwa pamaso pa Israyeli; uziwadula mitsindo akavalo ao, ndi kutentha agareta ao ndi moto.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 11

Onani Yoswa 11:6 nkhani