Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 11:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Monga Yehova adalamulira Mose mtumiki wace, momwemo Mose analamulira Yoswa; momwemonso anacita Yoswa; sanacotsapo mau amodzi pa zonse Yehova adalamulira Mose.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 11

Onani Yoswa 11:15 nkhani