Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 11:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa analanda midzi yonse ya mafumu awa, ndi mafumu ao omwe nawakantha ndi lupanga lakuthwa, nawaononga konse; monga Mose mtumiki wa Yehova adalamulira.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 11

Onani Yoswa 11:12 nkhani