Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 10:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Motero Yoswa anakantha dziko lonse, la kumapiri, la kumwela, la kucidikha, la kuzigwa, ndi mafumu ao onse; sanasiyapo ndi mmodzi yense; koma anaononga psiti zonse zampweya, monga Yehova Mulungu wa Israyeli adalamulira.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 10

Onani Yoswa 10:40 nkhani