Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 10:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

naulanda, naukantha ndi lupanga lakuthwa, ndi mfumu yace ndi midzi yace yonse, ndi amoyo onse anali m'mwemo, osasiyapo ndi mmodzi yense, monga mwa zonse anacitira Egiloni; koma anauononga konse, ndi amoyo onse anali m'mwemo.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 10

Onani Yoswa 10:37 nkhani