Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 10:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Horamu mfumu ya Gezere anakwera kudzathandiza Lakisi; ndipo Yoswa anamkantha iye ndi anthu ace mpaka sanamsiyira ndi mmodzi yense.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 10

Onani Yoswa 10:33 nkhani